Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 17:21 - Buku Lopatulika

21 (Koma Aatene onse ndi alendo akukhalamo anakhalitsa nthawi zao, osachita kanthu kena koma kunena kapena kumva cha tsopano.)

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 (Koma Aatene onse ndi alendo akukhalamo anakhalitsa nthawi zao, osachita kanthu kena koma kunena kapena kumva cha tsopano.)

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Ndiye kuti nzika za ku Atene ndi alendo okhala kumeneko, inali ngati ntchito nthaŵi zonse kumangomvera zatsopano ndi kumazifotokozera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Atene onse ndi alendo amene amakhala kumeneko samachita kanthu kena koma kufotokoza ndi kumvera fundo zatsopano.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 17:21
9 Mawu Ofanana  

Koma iwo amene anaperekeza Paulo anadza naye kufikira ku Atene; ndipo polandira iwo lamulo la kwa Silasi ndi Timoteo kuti afulumire kudza kwa iye ndi changu chonse, anachoka.


Pamene Paulo analindira iwo pa Atene, anavutidwa mtima pamene anaona mzinda wonse wadzala ndi mafano.


Pakuti ufika nazo kumakutu athu zachilendo: tifuna tsono kudziwa, izi zitani?


mu Frijiya, ndiponso mu Pamfiliya, mu Ejipito, ndi mbali za Libiya wa ku Kirene, ndi alendo ochokera ku Roma,


akuchita machawi, popeza masiku ali oipa.


Muyendere munzeru ndi iwo akunja, kuchita machawi nthawi ingatayike.


Ndipo aphunziraponso kuchita ulesi, aderuderu; koma osati ulesi wokha, komatunso alankhula zopanda pake, nachita mwina ndi mwina, olankhula zosayenera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa