Machitidwe a Atumwi 16:8 - Buku Lopatulika8 ndipo pamene anapita pambali pa Misiya, anatsikira ku Troasi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 ndipo pamene anapita pambali pa Misiya, anatsikira ku Troasi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Motero adapitirira Misiya nakafika ku Troasi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ndipo iwo anadutsa Musiya ndipo anapita ku Trowa. Onani mutuwo |