Machitidwe a Atumwi 16:7 - Buku Lopatulika7 pamene anafika kundunji kwa Misiya, anayesa kunka ku Bitiniya; ndipo Mzimu wa Yesu sanawaloleze; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 pamene anafika kundunji kwa Misiya, anayesa kunka ku Bitiniya; ndipo Mzimu wa Yesu sanawaloleza; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Pamene adafika ku malire a Misiya, adayesa kuloŵa m'dera la Bitiniya, koma Mzimu wa Yesu sadaŵalole. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Atafika ku malire a Musiya, anayesa kulowa ku Bituniya, koma Mzimu wa Yesu sunawalole kutero. Onani mutuwo |