Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 16:40 - Buku Lopatulika

40 Ndipo anatuluka m'ndendemo, nalowa m'nyumba ya Lidia: ndipo pamene anaona abale, anawasangalatsa, namuka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

40 Ndipo anatuluka m'ndendemo, nalowa m'nyumba ya Lidia: ndipo pamene anaona abale, anawasangalatsa, namuka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

40 Paulo ndi Silasi atatuluka m'ndende muja adapita kunyumba kwa Lidia. Kumeneko adaonana ndi abale, ndipo ataŵalimbikitsa, adachoka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

40 Paulo ndi Sila atatuluka mʼndende, anapita ku nyumba ya Lidiya, kumene anakumana ndi abale nawalimbikitsa. Kenaka anachoka.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 16:40
10 Mawu Ofanana  

Ndipo m'masiku awa anaimirira Petro pakati pa abale, nati (gulu la anthu losonkhana pamalo pomwe ndilo ngati zana limodzi ndi makumi awiri),


nalimbikitsa mitima ya ophunzira, nadandaulira iwo kuti akhalebe m'chikhulupiriro, ndi kuti tiyenera kulowa mu ufumu wa Mulungu ndi zisautso zambiri.


Ndipo anatimva mkazi wina dzina lake Lidia, wakugulitsa chibakuwa, wa kumzinda wa Tiatira, amene anapembedza Mulungu; mtima wake Ambuye anatsegula; kuti amvere zimene anazinena Paulo.


Ameneyo anamchitira umboni wabwino abale a ku Listara ndi Ikonio.


Ndipo m'mene anamasulidwa, anadza kwa anzao a iwo okha, nawauza zilizonse ansembe aakulu ndi akulu adanena nao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa