Machitidwe a Atumwi 16:38 - Buku Lopatulika38 Ndipo akapitao anafotokozera mauwo kwa oweruza; ndipo iwowo anaopa, pakumva kuti anali Aroma. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndipo akapitao anafotokozera mauwo kwa oweruza; ndipo iwowo anaopa, pakumva kuti anali Aroma. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Asilikali aja adapita kukaŵafotokozera akulu oweruza milandu aja mau ameneŵa. Pamene iwo aja adamva kuti ndi nzika za ufumu wa Aroma, adachita mantha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Asilikali aja anakafotokozera woweruza milandu ndipo pamene anamva kuti Paulo ndi Sila anali nzika za Chiroma, anachita mantha. Onani mutuwo |