Machitidwe a Atumwi 16:24 - Buku Lopatulika24 Pakumva iye kulamulira kotero anawaika m'chipinda cha m'kati, namangitsa mapazi ao m'zigologolo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Pakumva iye kulamulira kotero anawaika m'chipinda cha m'kati, namangitsa mapazi ao m'zigologolo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Chifukwa cha mau ameneŵa, woyang'anira ndende uja adakaŵatsekera m'chipinda cha m'katikati mwa ndende, namangirira mapazi ao m'matangadza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Chifukwa cha mawu amenewa woyangʼanira ndende anakawayika mʼchipinda chamʼkati mwa ndende, nawamangirira miyendo yawo mʼzigologolo. Onani mutuwo |