Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 16:21 - Buku Lopatulika

21 ndipo alalikira miyambo imene siiloleka ife kuilandira, kapena kuichita, ndife Aroma.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 ndipo alalikira miyambo imene siiloleka ife kuilandira, kapena kuichita, ndife Aroma.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Akuphunzitsa miyambo imene ife sitiloledwa kuivomera kapena kuitsata, popeza kuti ndife Aroma.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Ndipo akuphunzitsa miyambo imene ife Aroma sitiloledwa kuyilandira kapena kuyichita.”

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 16:21
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Hamani anati kwa mfumu Ahasuwero, Pali mtundu wina wa anthu obalalika ndi ogawanikana mwa mitundu ya anthu m'maiko onse a ufumu wanu, ndi malamulo ao asiyana nao a anthu onse, ndipo sasunga malamulo a mfumu; chifukwa chake mfumu siiyenera kuwaleka.


Pakuti miyambo ya anthu ili yachabe, pakuti wina adula mtengo m'nkhalango, ntchito ya manja a mmisiri ndi nkhwangwa.


Koma Afarisi, pakuona, anati kwa Iye, Tapenyani, ophunzira anu achita chosaloleka tsiku la Sabata.


pochokera kumeneko tinafika ku Filipi, mzinda wa ku Masedoniya, waukulu wa m'dzikomo, wa midzi ya Roma; ndipo tidagona momwemo masiku ena.


ndipo pamene adanka nao kwa oweruza, anati, Anthu awa avuta kwambiri mzinda wathu, ndiwo Ayuda,


makamaka popeza mudziwitsa miyambo yonse ndi mafunso onse a mwa Ayuda; chifukwa chake ndikupemphani mundimvere ine moleza mtima.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa