Machitidwe a Atumwi 16:20 - Buku Lopatulika20 ndipo pamene adanka nao kwa oweruza, anati, Anthu awa avuta kwambiri mzinda wathu, ndiwo Ayuda, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 ndipo pamene adanka nao kwa oweruza, anati, Anthu awa avuta kwambiri mudzi wathu, ndiwo Ayuda, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Atafika nawo kwa akulu oweruza milandu, adaŵauza kuti, “Anthu aŵa ndi Ayuda, ndipo akuvutitsa mumzinda mwathu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Anawabweretsa iwo kwa oweruza milandu ndipo anati, “Anthu awa ndi Ayuda, iwo akuvutitsa mu mzinda wathu. Onani mutuwo |