Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 16:11 - Buku Lopatulika

11 Chotero tinachokera ku Troasi m'ngalawa, m'mene tinalunjikitsa ku Samotrase, ndipo m'mawa mwake ku Neapoli;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Chotero tinachokera ku Troasi m'ngalawa, m'mene tinalunjikitsa ku Samotrase, ndipo m'mawa mwake ku Neapoli;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Kuchokera ku Troasi tidayenda m'chombo kulunjika ku chilumba cha Samotrase, ndipo m'maŵa mwake tidapitirira mpaka ku Neapoli.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Kuchokera ku Trowa tinakwera sitima ya pamadzi kupita ku Samotrake ndipo mmawa mwake tinapitirira mpaka ku Neapoli.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 16:11
5 Mawu Ofanana  

ndipo pamene anapita pambali pa Misiya, anatsikira ku Troasi.


Koma iwowa adatitsogolera, natilinda ku Troasi.


Ndipo kunali, titalekana nao ndi kukankha ngalawa, tinadza molunjika ku Kosi, ndi m'mawa mwake ku Rode, ndipo pochokerapo ku Patara;


Koma pamene ndinadza ku Troasi kudzalalikira Uthenga Wabwino wa Khristu, ndipo pamene padanditsegukira kwa ine pakhomo, mwa Ambuye,


Chofunda chija ndinachisiya ku Troasi kwa Karpo, udze nacho pakudza iwe, ndi mabuku, makamaka zikopa zija zolembedwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa