Machitidwe a Atumwi 16:10 - Buku Lopatulika10 Pamene anaona masomphenyawo, pomwepo tinayesa kutulukira kunka ku Masedoniya, poganizira kuti Mulungu anaitanira ife kulalikira Uthenga Wabwino kwa iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Pamene anaona masomphenyawo, pomwepo tinayesa kutulukira kunka ku Masedoniya, poganizira kuti Mulungu anaitanira ife kulalikira Uthenga Wabwino kwa iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Iye ataona zimenezi, nthaŵi yomweyo tidakonza ulendo wopita ku Masedoniya, chifukwa tidaadziŵadi kuti Mulungu ndiye watiwongolera kuti tikaŵalalikire Uthenga Wabwino anthu akumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Paulo ataona masomphenyawa, tinakonzeka kupita ku Makedoniya, kutsimikiza kuti Mulungu anatiyitana kuti tikalalikire Uthenga Wabwino. Onani mutuwo |