Machitidwe a Atumwi 15:30 - Buku Lopatulika30 Tsono pamene iwo anamuka anatsikira ku Antiokeya; ndipo anasonkhanitsa khamu, napereka kalatayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Tsono pamene iwo anamuka anatsikira ku Antiokeya; ndipo anasonkhanitsa khamu, napereka kalatayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Tsono otumidwa aja adanyamuka nakafika ku Antiokeya. Adasonkhanitsa mpingo wonse napereka kalata ija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Anthu aja anatumidwa ndipo anafika ku Antiokeya, kumene anasonkhanitsa mpingo pamodzi napereka kalatayo. Onani mutuwo |