Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 15:26 - Buku Lopatulika

26 anthu amene anapereka moyo wao chifukwa cha dzina la Yesu Khristu Ambuye wathu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 anthu amene anapereka moyo wao chifukwa cha dzina la Yesu Khristu Ambuye wathu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Amene adadzipereka kuti atumikire Ambuye athu Yesu Khristu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 anthu amene anapereka moyo wawo chifukwa cha dzina la Ambuye athu Yesu Khristu.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 15:26
8 Mawu Ofanana  

Koma Ayuda anakakamiza akazi opembedza ndi omveka, ndi akulu a mzindawo, nawautsira chizunzo Paulo ndi Barnabasi, ndipo anawapirikitsa iwo m'malire ao.


Ndipo anafika kumeneko Ayuda kuchokera ku Antiokeya ndi Ikonio; nakopa makamu, ndipo anamponya Paulo miyala, namguzira kunja kwa mzinda; namuyesa kuti wafa.


amene anapereka khosi lao chifukwa cha moyo wanga; amene ndiwayamika, si ine ndekha, komanso Mipingo yonse ya Ambuye ya kwa anthu amitundu;


Nanga ifenso tili m'moopsa bwanji nthawi zonse?


Zebuloni ndiwo anthu anataya moyo wao mpaka imfa, Nafutali yemwe poponyana pamisanje.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa