Machitidwe a Atumwi 15:21 - Buku Lopatulika21 Pakuti Mose, kuyambira pa mibadwo yakale ali nao m'mizinda yonse amene amlalikira, akuwerenga mau ake m'masunagoge masabata onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Pakuti Mose, kuyambira pa mibadwo yakale ali nao m'midzi yonse amene amlalikira, akuwerenga mau ake m'masunagoge masabata onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Paja kuyambira kalekale mu mzinda uliwonse muli anthu ophunzitsa Malamulo a Mose, ndipo amaŵerenga mau ake m'nyumba zamapemphero pa tsiku la Sabata lililonse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Pakuti malamulo a Mose akhala akulalikidwa mu mzinda uliwonse, kuyambira kalekale ndipo amawerengedwa mʼMasunagoge tsiku la Sabata.” Onani mutuwo |