Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 15:16 - Buku Lopatulika

16 Zikatha izo ndidzabwera, ndidzamanganso chihema cha Davide, chimene chinagwa; ndidzamanganso zopasuka zake, ndipo ndidzachiimikanso:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Zikatha izo ndidzabwera, ndidzamanganso chihema cha Davide, chimene chinagwa; ndidzamanganso zopasuka zake, ndipo ndidzachiimikanso:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 “ ‘Zitatha zimenezi ndidzabwerera, ndidzamanganso nyumba ya Davide imene idagwa. Ndidzamanganso zopasuka zake, ndi kuikonzanso.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 “ ‘Zitatha izi Ine ndidzabwerera ndipo ndidzamanganso nyumba ya Davide imene inagwa. Ndidzakonzanso malo amene anagumuka, ndi kuyimanganso,

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 15:16
12 Mawu Ofanana  

Ndipo pakuona Aisraele onse kuti mfumu siinawamvere iwo, anthuwo anayankha mfumu, Tili naye chiyani Davide? Inde tilibe cholowa m'mwana wa Yese; tiyeni kwathu Aisraele inu; yang'aniranitu nyumba yako, Davide. Momwemo Aisraele anachoka kunka ku mahema ao.


Ndipo padzakhala kuti nditazula iwo, ndidzabwera, ndipo ndidzawachitira chisoni; ndipo ndidzabwezanso iwo, yense ku cholowa chake, ndi yense kudziko lake.


Ndipo kudzachitika m'dziko lonse, ati Yehova, magawo awiri m'menemo adzalikhidwa nadzafa; koma gawo lachitatu lidzasiyidwa m'mwemo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa