Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 14:16 - Buku Lopatulika

16 m'mibadwo yakale Iye adaleka mitundu yonse iyende m'njira mwao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 m'mibadwo yakale Iye adaleka mitundu yonse iyende m'njira mwao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Kale Iye adaalekerera anthu a mitundu yonse kuti azitsata njira zaozao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Kale Iye analola anthu a mitundu ina yonse kutsata njira zawozawo.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 14:16
10 Mawu Ofanana  

Sanatero nao anthu a mtundu wina; ndipo za maweruzo ake, sanawadziwe. Aleluya.


Potero ndinawaperekera kuuma mtima kwao, ayende monga mwa uphungu waowao.


Efuremu waphatikana ndi mafano, mlekeni.


Pakuti mitundu yonse ya anthu idzayenda, wonse m'dzina la mulungu wake, ndipo ife tidzayenda m'dzina la Yehova Mulungu wathu kunthawi yonka muyaya.


Nthawi za kusadziwako tsono Mulungu analekerera; koma tsopanotu alinkulamulira anthu onse ponseponse atembenuke mtima;


Ndipo monga iwo anakana kukhala naye Mulungu m'chidziwitso chao, anawapereka Mulungu kumtima wokanika, kukachita zinthu zosayenera;


amene Mulungu anamuika poyera akhale chotetezera mwa chikhulupiriro cha m'mwazi wake, kuti aonetse chilungamo chake, popeza Mulungu m'kulekerera kwake analekerera machimo ochitidwa kale lomwe;


kuti nthawi ija munali opanda Khristu, alendo a padera ndi mbumba ya Israele, ndi alendo alibe kanthu ndi mapangano a malonjezano, opanda chiyembekezo, ndi opanda Mulungu m'dziko lapansi.


Pakuti nthawi yapitayi idakufikirani kuchita chifuniro cha amitundu, poyendayenda inu m'kukhumba zonyansa, zilakolako, maledzero, madyerero, maimwaimwa, ndi kupembedza mafano kosaloleka;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa