Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 14:12 - Buku Lopatulika

12 Ndipo anamutcha Barnabasi, Zeusi; ndi Paulo, Heremesi, chifukwa anali wotsogola kunena.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndipo anamutcha Barnabasi, Zeusi; ndi Paulo, Heremesi, chifukwa anali wotsogola kunena.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Motero Barnabasi adamutcha Zeusi ndipo Paulo adamutcha Heremesi, chifukwa ndiye ankatsogola polankhula.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Barnaba anamutcha Zeusi ndipo Paulo anamutcha Herimesi chifukwa ndiye amatsogolera kuyankhula.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 14:12
3 Mawu Ofanana  

Pamene makamu anaona chimene anachita Paulo, anakweza mau ao, nati m'chinenero cha Likaoniya, Milungu yatsikira kwa ife monga anthu.


Koma wansembe wa Zeusi wa kumaso kwa mzinda, anadza nazo ng'ombe ndi maluwa kuzipata, nafuna kupereka nsembe pamodzi ndi makamu.


Ndipo pamene mlembi adatontholetsa khamulo, anati, Amuna a Efeso inu, munthuyu ndani wosadziwa kuti mzinda wa Aefeso ndiwo wosungira Kachisi wa Aritemi wamkulu, ndi fano lidachokera kwa Zeusi?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa