Machitidwe a Atumwi 14:11 - Buku Lopatulika11 Pamene makamu anaona chimene anachita Paulo, anakweza mau ao, nati m'chinenero cha Likaoniya, Milungu yatsikira kwa ife monga anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Pamene makamu anaona chimene anachita Paulo, anakweza mau ao, nati m'chinenero cha Likaoniya, Milungu yatsikira kwa ife monga anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Pamene anthu onse aja adaona zimene Paulo adachita, adafuula m'Chilikaoniya kuti, “Yatitsikira milungu yooneka ngati anthu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Gulu la anthu litaona zimene Paulo anachitazi, linafuwula mʼChilukaoniya kuti, “Milungu yatitsikira yooneka ngati anthu!” Onani mutuwo |