Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 14:10 - Buku Lopatulika

10 anati ndi mau aakulu, Taimirira. Ndipo iyeyu anazunzuka, nayenda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 anati ndi mau akulu, Taimirira. Ndipo iyeyu anazunzuka, nayenda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 adanena mokweza mau kuti, “Wongola miyendo yako, imirira.” Pomwepo munthuyo adadzambatuka nkuyamba kuyenda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Ndipo Paulo anamuyitana mofuwula nati, “Imirira!” Atamva zimenezi, munthuyo anayimirira, nayamba kuyenda.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 14:10
8 Mawu Ofanana  

Pamenepo wopunduka adzatumpha ngati nswala, ndi lilime la wosalankhula lidzaimba; pakuti m'chipululu madzi adzatuluka, ndi mitsinje m'dziko loti see.


Ndipo anayandikira, nakhudza chithatha; ndipo akumnyamulawo anaima. Ndipo Iye anati, Mnyamata iwe, ndinena ndi iwe, Tauka.


Indetu, indetu, ndinena kwa inu, Wokhulupirira Ine, ntchito zimene ndichita Ine adzazichitanso iyeyu; ndipo adzachita zoposa izi; chifukwa ndipita Ine kwa Atate.


koma iye wakumwa madzi amene Ine ndidzampatsa sadzamva ludzu nthawi zonse; koma madzi amene Ine ndidzampatsa adzakhala mwa iye kasupe wa madzi otumphukira kumoyo wosatha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa