Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 13:44 - Buku Lopatulika

44 Ndipo Sabata linalo udasonkhana pamodzi ngati mzinda wonse kumva mau a Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

44 Ndipo Sabata linalo udasonkhana pamodzi ngati mudzi wonse kumva mau a Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

44 Pa tsiku la Sabata linalo pafupi anthu onse amumzindamo adasonkhana kuti amve mau a Ambuye.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

44 Pa Sabata linalo pafupifupi anthu onse a mu mzindawo anasonkhana kudzamva Mawu a Ambuye.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 13:44
6 Mawu Ofanana  

Ndodo yachifumu siidzachoka mwa Yuda, kapena wolamulira pakati pa mapazi ake, kufikira atadza Silo; ndipo anthu adzamvera iye.


Anthu anu adzadzipereka eni ake tsiku la chamuna chanu: M'moyera mokometsetsa, mobadwira matanda kucha, muli nao mame a ubwana wanu.


Ndipo padzakhala tsiku lomwelo, kuti muzu wa Yese umene uima ngati mbendera ya mitundu ya anthu, amitundu adzafunafuna uwu; ndipo popuma pake padzakhala ulemerero.


Ndani awa amene auluka ngati mtambo, ndi monga nkhunda kumazenera ao?


Ndipo onani, mzinda wonse unatulukira kukakumana naye Yesu, ndipo m'mene anamuona Iye, anampempha kuti achoke m'malire ao.


Koma iwowa, atapita pochokera ku Perga anafika ku Antiokeya wa mu Pisidiya; ndipo analowa m'sunagoge tsiku la Sabata, nakhala pansi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa