Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 13:24 - Buku Lopatulika

24 Yohane atalalikiratu, asanafike Iye, ubatizo wa kulapa kwa anthu onse a Israele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Yohane atalalikiratu, asanafike Iye, ubatizo wa kulapa kwa anthu onse a Israele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Iyeyo asanayambe ntchito, Yohane ankalalikira Aisraele onse kuti atembenuke mtima ndi kubatizidwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Yesu asanabwere, Yohane analalikira kwa anthu onse Aisraeli za kutembenuka mtima ndi ubatizo.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 13:24
12 Mawu Ofanana  

Chiyambi chake cha Uthenga Wabwino wa Yesu Khristu, Mwana wa Mulungu.


Eya, ndipo iwetu kamwanawe, udzanenedwa mneneri wa Wamkulukulu; pakuti udzatsogolera Ambuye, kukonza njira zake.


kuyambira ubatizo wa Yohane, kufikira tsiku lija anatengedwa kunka Kumwamba kutisiya ife, mmodzi wa awa akhale mboni ya kuuka kwake pamodzi ndi ife.


mauwo muwadziwa inu, adadzawo ku Yudeya lonse, akuyamba ku Galileya, ndi ubatizo umene Yohane anaulalikira;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa