Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 12:25 - Buku Lopatulika

25 Ndipo Barnabasi ndi Saulo anabwera kuchokera ku Yerusalemu m'mene adatsiriza utumiki wao, natenga Yohane wonenedwanso Marko amuke nao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Ndipo Barnabasi ndi Saulo anabwera kuchokera ku Yerusalemu m'mene adatsiriza utumiki wao, natenga Yohane wonenedwanso Marko amuke nao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Tsono Barnabasi ndi Saulo atakwaniritsa zimene adaaŵatumira ku Yerusalemu, adabwerako. Adatengako Yohane wotchedwa Marko uja.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Barnaba ndi Saulo atamaliza ntchito yawo anachoka ku Yerusalemu, atatenga Yohane wotchedwanso Marko.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 12:25
10 Mawu Ofanana  

Ndipo m'mene adalingirirapo, anadza kunyumba ya Maria amake wa Yohane wonenedwanso Marko; pamenepo ambiri adasonkhana pamodzi, ndipo analikupemphera.


Koma Paulo ndi Barnabasi anakhalabe mu Antiokeya, nalinkuphunzitsa, ndi kulalikira mau a Ambuye pamodzi ndi ena ambiri.


Ndipo Barnabasi anafuna kumtenga Yohane uja, wotchedwa Marko


Ndipo Yosefe, wotchedwa ndi atumwi Barnabasi (ndilo losandulika mwana wa chisangalalo), Mlevi, fuko lake la ku Kipro,


Aristariko wam'ndende mnzanga akupatsani moni, ndi Marko, msuweni wa Barnabasi (amene munalandira zolamulira za kwa iye; akafika kwanu, mumlandire iye),


Luka yekha ali pamodzi ndi ine. Umtenge Marko, adze pamodzi ndi iwe; pakuti ayenera kunditumikira.


ateronso, Marko, Aristariko, Dema, Luka, antchito anzanga.


Iye wa ku Babiloni wosankhidwa pamodzi nanu akukupatsani moni; ateronso Marko mwana wanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa