Machitidwe a Atumwi 12:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo anthu osonkhanidwawo anafuula, Ndiwo mau a Mulungu, si a munthu ai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo anthu osonkhanidwawo anafuula, Ndiwo mau a Mulungu, si a munthu ai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Anthuwo adanena mokweza mau kuti, “Ameneŵa ndi mau a mulungu, osati a munthu ai.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Anthuwo anafuwula nati, “Amenewa ndi mawu a mulungu osati a munthu ayi.” Onani mutuwo |
Akulu onse a ufumuwo, ndi akazembe ndi akalonga, mandoda, ndi ziwanga, anapangana kukhazika lemba lachifumu, ndi kuikapo choletsa cholimba, kuti aliyense akapempha kanthu kwa mulungu aliyense, kapena kwa munthu aliyense masiku makumi atatu, osati kwa inu nokha, mfumu, adzaponyedwa m'dzenje la mikango.