Machitidwe a Atumwi 12:18 - Buku Lopatulika18 Koma kutacha, panali phokoso lalikulu mwa asilikali, Petro wamuka kuti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Koma kutacha, panali phokoso lalikulu mwa asilikali, Petro wamuka kuti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Kutacha, asilikali aja adasokonezeka kwabasi nati, “Petro wapita kuti?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Pamene kunacha kunali phokoso lalikulu pakati pa asilikali, iwo anafunsa kuti, “Kodi chamuchitikira Petro ndi chiyani?” Onani mutuwo |