Machitidwe a Atumwi 12:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo pozindikira mau ake a Petro, chifukwa cha kukondwera sanatsegule pakhomo, koma anathamanga nalowanso, nawauza kuti Petro alikuima pakhomo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo pozindikira mau ake a Petro, chifukwa cha kukondwera sanatsegula pakhomo, koma anathamanga nalowanso, nawauza kuti Petro alikuima pakhomo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Atazindikira liwu lake kuti ndi la Petro, adakondwa kwambiri, kotero kuti sadatsekule chitsekocho, koma adathamangiranso m'kati nakawuza ena aja kuti, “Petro ali pakhomopa!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Atazindikira mawu a Petro anakondwa kwambiri ndipo anabwerera osatsekula ndipo anafuwula kuti, “Petro ali pa khomopa!” Onani mutuwo |