Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 12:13 - Buku Lopatulika

13 Ndipo m'mene anagogoda pa chitseko cha pakhomo, anadza kudzavomera mdzakazi, dzina lake Roda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndipo m'mene anagogoda pa chitseko cha pakhomo, anadza kudzavomera mdzakazi, dzina lake Roda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Pamene Petro adagogoda pa chitseko chapakhomo, mtsikana wina, dzina lake Roda, adabwera kuti amtsekulire.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Petro anagogoda pa chitseko cha panja, ndipo mtsikana wantchito dzina lake Roda anabwera kuti adzatsekule chitseko.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 12:13
4 Mawu Ofanana  

Ndipo pamene iye anatuluka kunka kuchipata, mkazi wina anamuona, nati kwa iwo a pomwepo, Uyonso anali ndi Yesu Mnazarayo.


Pamene atauka mwini nyumba natseka pakhomo, ndipo inu mudzayamba kuima pabwalo, ndi kugogoda pachitseko, ndi kunena, Ambuye titsegulireni ife; ndipo Iye adzayankha nadzati ndi inu, Sindidziwa inu kumene muchokerako;


Koma Petro anakhala chigogodere; ndipo m'mene adamtsegulira, anamuona iye, nadabwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa