Machitidwe a Atumwi 12:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo m'mene adalingirirapo, anadza kunyumba ya Maria amake wa Yohane wonenedwanso Marko; pamenepo ambiri adasonkhana pamodzi, ndipo analikupemphera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo m'mene adalingirirapo, anadza kunyumba ya Maria amake wa Yohane wonenedwanso Marko; pamenepo ambiri adasonkhana pamodzi, ndipo analikupemphera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Atazindikira zimenezi, adapita kunyumba kwa Maria, amai ake a Yohane wotchedwanso Marko. Anthu ambiri anali atasonkhana kumeneko akupemphera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Atazindikira zimenezi anapita ku nyumba ya Mariya amayi ake a Yohane, wotchedwanso Marko, kumene kunasonkhana anthu ambiri ndipo amapemphera. Onani mutuwo |