Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 12:1 - Buku Lopatulika

1 Koma nyengo imeneyo Herode mfumu anathira manja ena a mu Mpingo kuwachitira zoipa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Koma nyengo imeneyo Herode mfumu anathira manja ena a m'Mpingo kuwachitira zoipa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Pafupi ngati nthaŵi imeneyo mfumu Herode adagwira ena a mu Mpingo kuti aŵazunze.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Inali nthawi yomweyi imene mfumu Herode anamanga ena a mu mpingo ndi cholinga chakuti awazunze.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 12:1
13 Mawu Ofanana  

Pakuti ndodo yachifumu ya choipa siidzapumula pa gawo la olungama; kuti olungama asatulutse dzanja lao kuchita chosalungama.


Nthawi imeneyo Herode mfumu anamva mbiri ya Yesu,


Pakuti Herode adamgwira Yohane, nammanga, namuika m'nyumba yandende chifukwa cha Herodiasi, mkazi wa mbale wake Filipo.


Koma pakufika tsiku la kubadwa kwake kwa Herode, mwana wamkazi wa Herodiasi anavina pakati pao, namkondweretsa Herode.


Pamenepo adzakuperekani kunsautso, nadzakuphani; ndipo anthu a mitundu yonse adzadana nanu, chifukwa cha dzina langa.


Masiku onse, pamene ndinali ndi inu mu Kachisi, simunatanse manja anu kundigwira: koma nyengo ino ndi yanu, ndipo ulamuliro wa mdima ndi wanu.


Kumbukirani mau amene Ine ndinanena kwa inu, Kapolo sali wamkulu ndi mbuye wake. Ngati anandilondalonda Ine, adzakulondalondani inunso; ngati anasunga mau anga, adzasunga anunso.


Adzakutulutsani m'masunagoge, koma ikudza nthawi imene yense wakupha inu adzayesa kuti atumikira Mulungu.


ichonso anachita, natumiza kwa akulu mwa dzanja la Barnabasi ndi Saulo.


Ndipo adapha ndi lupanga Yakobo mbale wa Yohane.


m'mene mutambasula dzanja lanu kukachiritsa; ndi kuti zizindikiro ndi zozizwa zichitidwe mwa dzina la Mwana wanu wopatulika Yesu.


Pamenepo ndipo Mpingo wa mu Yudeya yense ndi Galileya ndi Samariya unali nao mtendere, nukhazikika; ndipo unayenda m'kuopa kwa Ambuye ndi m'chitonthozo cha Mzimu Woyera, nuchuluka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa