Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 10:44 - Buku Lopatulika

44 Petro ali chilankhulire, Mzimu Woyera anagwa pa onse akumva mauwo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

44 Petro ali chilankhulire, Mzimu Woyera anagwa pa onse akumva mauwo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

44 Petro akulankhulabe, Mzimu Woyera adaŵatsikira anthu onse amene ankamva mauwo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

44 Petro akuyankhulabe mawu amenewa, Mzimu Woyera unatsikira pa onse amene amamva uthengawo.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 10:44
7 Mawu Ofanana  

Kodi pali munthu akhoza kuletsa madzi, kuti asabatizidwe awa, amene alandira Mzimu Woyera ngatinso ife?


Ndipo m'mene ndinayamba kulankhula, Mzimu Woyera anawagwera, monga anatero ndi ife poyamba paja.


Ndipo Mulungu, amene adziwa mtima, anawachitira umboni; nawapatsa Mzimu Woyera, monga anatipatsa ife;


Ndipo pamene Paulo anaika manja ake pa iwo, Mzimu Woyera anadza pa iwo; ndipo analankhula ndi malilime, nanenera.


Ndipo m'mene adapemphera iwo, panagwedezeka pamalo pamene adasonkhanirapo; ndipo anadzazidwa onse ndi Mzimu Woyera, nalankhula mau a Mulungu molimbika mtima.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa