Machitidwe a Atumwi 10:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo ife ndife mboni za zonse adazichita m'dziko la Ayuda ndi mu Yerusalemu; amenenso anamupha, nampachika pamtengo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo ife ndife mboni za zonse adazichita m'dziko la Ayuda ndi m'Yerusalemu; amenenso anamupha, nampachika pamtengo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Ife ndife mboni za zonse zimene Iye adachita mu Yerusalemu ndi m'dziko lonse la Ayuda. Iwo adamupha pakumpachika pa mtanda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 “Ife ndife mboni za zonse zimene anachita mʼdziko la Ayuda ndiponso ku Yerusalemu. Anamupha Iye pakumupachika pa mtengo, Onani mutuwo |