Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 10:26 - Buku Lopatulika

26 Koma Petro anamuutsa iye, nanena, Nyamuka; inenso ndine munthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Koma Petro anamuutsa iye, nanena, Nyamuka; inenso ndine munthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Koma Petro adamuimiritsa nati, “Iyai, imirirani, inenso ndine munthu chabe.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Koma Petro anamuyimiritsa nati, “Imirira, inenso ndine munthu ngati iwe.”

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 10:26
8 Mawu Ofanana  

Ine ndine Yehova; dzina langa ndi lomweli; ndipo ulemerero wanga Ine sindidzapereka kwa wina, ngakhale kunditamanda kwa mafano osemedwa.


Inde dzanja langa linakhazika maziko a dziko lapansi, ndi dzanja langa lamanja linafunyulula m'mwamba; pakuziitana Ine ziimirira pamodzi.


Pomwepo Yesu ananena kwa iye, Choka Satana, pakuti kwalembedwa, Ambuye Mulungu wako udzamgwadira, ndipo Iye yekhayekha udzamlambira.


Ndipo adzachilambira onse akukhala padziko, amene dzina lao silinalembedwe m'buku la moyo la Mwanawankhosa, wophedwa kuyambira makhazikidwe a dziko lapansi.


Ndipo ndinagwa pa mapazi ake kumlambira iye. Ndipo ananena ndi ine, Tapenya, usatero; ine ndine kapolo mnzako, ndi mnzao wa abale ako akukhala nao umboni wa Yesu; lambira Mulungu: pakuti umboni wa Yesu ndiwo Mzimu wa chinenero.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa