Machitidwe a Atumwi 10:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo panali pakulowa Petro, Kornelio anakomana naye, nagwa pa mapazi ake, namlambira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo panali pakulowa Petro, Kornelio anakomana naye, nagwa pa mapazi ake, namlambira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Pamene Petro ankati aziloŵa, Kornelio adadzakumana naye, nadzigwetsa kumapazi kwake, namuŵeramira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Petro akulowa mʼnyumba, Korneliyo anakumana naye ndipo anadzigwetsa pa mapazi ake namulambira. Onani mutuwo |