Machitidwe a Atumwi 10:23 - Buku Lopatulika23 Pamenepo anawalowetsa nawachereza. Ndipo m'mawa mwake ananyamuka natuluka nao, ndi ena a abale a ku Yopa anamperekeza iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Pamenepo anawalowetsa nawachereza. Ndipo m'mawa mwake ananyamuka natuluka nao, ndi ena a abale a ku Yopa anamperekeza iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Pamenepo Petro adaŵaloŵetsa m'nyumba, naŵasamala. M'maŵa mwake adanyamuka napita nawo, ndipo abale ena a ku Yopa adamperekeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Pamenepo Petro anawalowetsa mʼnyumba ndipo anawasamala ngati alendo ake. Mmawa mwake Petro ananyamuka napita nawo ndipo abale ena a ku Yopa anapita naye pamodzi. Onani mutuwo |