Machitidwe a Atumwi 1:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo anaimikapo awiri, Yosefe wotchedwa Barsabasi, amene anatchedwanso Yusto, ndi Matiasi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo anaimikapo awiri, Yosefe wotchedwa Barsabasi, amene anatchedwanso Yusto, ndi Matiasi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Pamenepo iwo adatchula maina aŵiri: Yosefe amene ankamutcha Barsabasi (dzina lake lina ndi Yusto,) ndi Matiasi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Pamenepo anasankha anthu awiri, Yosefe wotchedwa Barsaba (wodziwikanso kuti Yusto) ndi Matiyasi. Onani mutuwo |