Machitidwe a Atumwi 1:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo pakukhala iwo chipenyerere kumwamba pomuka Iye, taonani, amuna awiri ovala zoyera anaimirira pambali pao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo pakukhala iwo chipenyerere kumwamba pomuka Iye, taonani, amuna awiri ovala zoyera anaimirira pambali pao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 M'mene atumwi aja ankayang'anitsitsabe kumwamba, Iye akupita, mwadzidzidzi anthu aŵiri ovala zoyera adaimirira pambali pao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Yesu akukwera kumwamba, ophunzira ake anayangʼanitsitsa ndi chidwi mʼmitambo. Mwadzidzidzi anaona anthu awiri ovala zoyera atayimirira pambali pawo. Onani mutuwo |