Luka 9:49 - Buku Lopatulika49 Ndipo Yohane anayankha nati, Ambuye, tinaona wina alikutulutsa ziwanda m'dzina lanu; ndipo tinamletsa, chifukwa satsatana nafe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201449 Ndipo Yohane anayankha nati, Ambuye, tinaona wina alikutulutsa ziwanda m'dzina lanu; ndipo tinamletsa, chifukwa satsatana nafe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa49 Yohane adati, “Aphunzitsi, ife tinaona munthu wina akutulutsa mizimu yoipa potchula dzina lanu, ndiye ife tinayesa kumletsa, chifukwa sayenda nafe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero49 Yohane anati, “Ambuye, ife tinaona munthu akutulutsa ziwanda mʼdzina lanu ndipo tinayesa kumuletsa, chifukwa iyeyo si mmodzi wa ife.” Onani mutuwo |