Luka 9:45 - Buku Lopatulika45 Koma iwo sanadziwitse mau awa, ndipo anabisidwa kwa iwo, kuti asawadziwe; ndipo anaopa kumfunsa za mau awa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Koma iwo sanadziwitse mau awa, ndipo anabisidwa kwa iwo, kuti asawadziwe; ndipo anaopa kumfunsa za mau awa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Iwowo sadamvetse mau ameneŵa. Anali obisika kwa iwo, kotero kuti sadaŵamvetsetse. Koma ankaopa kumufunsa zimenezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Koma iwo sanazindikire zimene amatanthauza. Izi zinawadabwitsa kotero sanathe kuzimvetsa ndipo anaopa kumufunsa. Onani mutuwo |