Luka 9:37 - Buku Lopatulika37 Ndipo panali, m'mawa mwake, atatsika m'phiri, khamu lalikulu la anthu linakomana naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Ndipo panali, m'mawa mwake, atatsika m'phiri, khamu lalikulu la anthu linakomana naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 M'maŵa mwake Yesu ndi ophunzira atatuwo adatsika kuphiri kuja, ndipo anthu ambirimbiri adadzamchingamira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Mmawa mwake, akutsika ku phiri, anthu ambiri anakumana naye. Onani mutuwo |