Luka 8:50 - Buku Lopatulika50 Koma Yesu anamva, namyankha, kuti, Usaope; khulupirira kokha, ndipo iye adzapulumutsidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201450 Koma Yesu anamva, namyankha, kuti, Usaope; khulupirira kokha, ndipo iye adzapulumutsidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa50 Yesu atamva mauwo adauza Yairo kuti, “Musaope ai, inu mungokhulupira, ndipo mwanayo akhalanso bwino.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero50 Atamva zimenezi, Yesu anati kwa Yairo, “Usachite mantha, ingokhulupirira basi ndipo adzachiritsidwa.” Onani mutuwo |