Luka 8:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo iwo anakocheza kudooko ku dziko la Agerasa, ndilo lopenyana ndi Galileya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo iwo anakocheza kudooko ku dziko la Agerasa, ndilo lopenyana ndi Galileya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Iwo adafika ku dziko la Ageregesa, limene lidapenyana ndi Galileya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Iwo anawolokera ku chigawo cha Gerasa chimene chili tsidya lina la nyanja kuchokera ku Galileya. Onani mutuwo |