Luka 6:24 - Buku Lopatulika24 Koma tsoka inu eni chuma! Chifukwa mwalandira chisangalatso chanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Koma tsoka inu eni chuma! Chifukwa mwalandira chisangalatso chanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 “Koma ndinu atsoka, anthu achumanu, chifukwa mwalandiriratu zokusangalatsani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 “Ndinu atsoka, anthu olemera, popeza mwalandiriratu zokusangalatsani. Onani mutuwo |