Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 4:33 - Buku Lopatulika

33 Ndipo m'sunagoge munali munthu, wokhala nacho chiwanda chonyansa; nafuula ndi mau olimba, kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

33 Ndipo munali m'sunagoge munthu, wokhala nacho chiwanda chonyansa; nafuula ndi mau olimba, kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

33 M'nyumba yamapempheroyo munali munthu wogwidwa ndi mzimu womuipitsa. Adalankhula mokuwa kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

33 Mʼsunagogemo munali munthu wogwidwa ndi mzimu woyipa. Iye analira ndi mawu akulu, akuti

Onani mutuwo Koperani




Luka 4:33
3 Mawu Ofanana  

Ndipo pomwepo panali munthu m'sunagoge mwao ali ndi mzimu wonyansa; ndipo anafuula iye.


chifukwa mau ake anali ndi ulamuliro.


Ha! Tili ndi chiyani ndi Inu, Yesu wa ku Nazarete? Kodi munadza kutiononga ife? Ndikudziwani Inu muli yani, ndinu Woyera wake wa Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa