Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 24:40 - Buku Lopatulika

40 Ndipo m'mene ananena ichi, anawaonetsera iwo manja ake ndi mapazi ake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

40 Ndipo m'mene ananena ichi, anawaonetsera iwo manja ake ndi mapazi ake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

40 Atanena zimenezi adaŵaonetsa manja ake ndi mapazi ake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

40 Iye atanena izi anawaonetsa manja ake ndi mapazi ake.

Onani mutuwo Koperani




Luka 24:40
4 Mawu Ofanana  

Penyani manja anga ndi mapazi anga, kuti Ine ndine mwini: ndikhudzeni, ndipo penyani; pakuti mzimu ulibe mnofu ndi mafupa, monga muona ndili nazo Ine.


Koma pokhala iwo chikhalire osakhulupirira chifukwa cha chimwemwe, nalikuzizwa, anati kwa iwo, Muli nako kanthu kakudya kuno?


Ndipo pamene adanena ichi, anaonetsa iwo manja ake ndi nthiti zake. Pamenepo ophunzira anakondwera pakuona Ambuye.


Pomwepo ananena kwa Tomasi, Bwera nacho chala chako kuno, nuone manja anga, ndipo bwera nalo dzanja lako, nuliike kunthiti yanga, ndipo usakhale wosakhulupirira, koma wokhulupirira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa