Luka 24:35 - Buku Lopatulika35 Ndipo iwo anawafotokozera za m'njira, ndi umo anadziwika nao m'kunyema kwa mkate. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndipo iwo anawafotokozera za m'njira, ndi umo anadziwika nao m'kunyema kwa mkate. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Tsono nawonso aŵiri aja adafotokoza zimene zidaachitika panjira paja, ndiponso m'mene iwo adaamzindikirira pamene Iye ankanyema buledi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Kenaka awiriwo anawawuza zimene zinachitika pa njira, ndi mmene iwo anamudziwira Yesu, Iye atanyema buledi. Onani mutuwo |