Luka 23:49 - Buku Lopatulika49 Ndipo omdziwa Iye onse, ndi akazi amene adamtsata kuchokera ku Galileya, anaima kutali, naona zinthu izi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201449 Ndipo omdziwa Iye onse, ndi akazi amene adamtsata kuchokera ku Galileya, anaima kutali, naona zinthu izi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa49 Anthu onse amene ankadziŵana ndi Yesu, ndiponso azimai amene adaamtsatira kuchokera ku Galileya, adaima patali nkumaona zimenezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero49 Koma onse amene anamudziwa Iye, kuphatikiza amayi amene anamutsatira kuchokera ku Galileya, anayimirira akuona zinthu izi. Onani mutuwo |