Luka 23:47 - Buku Lopatulika47 Ndipo pamene kenturiyo anaona chinachitikacho, analemekeza Mulungu, nanena, Zoonadi munthu uyu anali wolungama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Ndipo pamene kenturiyo anaona chinachitikacho, analemekeza Mulungu, nanena, Zoonadi munthu uyu anali wolungama. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 Mkulu wa asilikali ataona zimene zidaachitikazo, adatamanda Mulungu, adati, “Ndithudi munthuyu adaalidi wosalakwa konse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 Kenturiyo, ataona zimene zinachitikazi, analemekeza Mulungu ndipo anati, “Zoonadi, uyu anali munthu wolungama.” Onani mutuwo |