Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 23:45 - Buku Lopatulika

45 Ndipo nsalu yotchinga ya mu Kachisi inang'ambika pakati.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

45 Ndipo nsalu yotchinga ya m'Kachisi inang'ambika pakati.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

45 dzuŵa litangoti bii kuda. Pamenepo chinsalu chochinga chija cha m'Nyumba ya Mulungu chidang'ambika pakatimpakati.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

45 pakuti dzuwa linaleka kuwala. Ndipo chinsalu cha mʼNyumba ya Mulungu chinangʼambika pakati.

Onani mutuwo Koperani




Luka 23:45
9 Mawu Ofanana  

Ndipo anaomba nsalu yotchinga ya thonje lamadzi, ndi lofiira, ndi lofiirira, ndi bafuta wa thonje losansitsa, naomberamo akerubi.


Ndipo onani, chinsalu chotchinga cha mu Kachisi chinang'ambika pakati, kuchokera kumwamba kufikira pansi; ndipo dziko linagwedezeka, ndi miyala inang'ambika;


Ndipo chinsalu chotchinga cha mu Kachisi chinang'ambika pakati, kuyambira kumwamba kufikira pansi.


chimene tili nacho ngati nangula wa moyo, chokhazikika ndi cholimbanso, ndi chakulowa m'katikati mwa chophimba;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa