Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Luka 23:36 - Buku Lopatulika

36 Ndipo asilikalinso anamnyoza, nadza kwa Iye, nampatsa vinyo wosasa,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 Ndipo asilikalinso anamnyoza, nadza kwa Iye, nampatsa vinyo wosasa,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Nawonso asilikali adayamba kumseka. Adadza pafupi ndi Iye, nampatsa vinyo wosasa kuti amwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 Asilikalinso anabwera ndi kumunyoza Iye. Iwo anamupatsa vinyo wosasa,

Onani mutuwo Koperani




Luka 23:36
8 Mawu Ofanana  

Ndipo anandipatsa ndulu ikhale chakudya changa; nandimwetsa vinyo wosasa pomva ludzu ine.


anamwetsa Iye vinyo wosakaniza ndi ndulu; ndipo Iye, m'mene analawa, sanafune kumwa.


Ndipo pomwepa mmodzi wa iwo anathamanga, natenga chinkhupule, nachidzaza ndi vinyo wosasa, nachiika pabango, namwetsa Iye.


Ndipo anathamanga wina, nadzaza chinkhupule ndi vinyo wosasa, nachiika pabango, namwetsa Iye, nanena, Lekani; tione ngati Eliya adza kudzamtsitsa.


Ndipo Herode ndi asilikali ake anampeputsa Iye, namnyoza, namveka Iye chofunda chonyezimira, nambwezera kwa Pilato.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa