Luka 23:29 - Buku Lopatulika29 Chifukwa taonani masiku alinkudza, pamene adzati, Odala ali ouma ndi mimba yosabala, ndi mawere osayamwitsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Chifukwa taonani masiku alinkudza, pamene adzati, Odala ali ouma ndi mimba yosabala, ndi mawere osayamwitsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Pakuti masiku akubwera pamene anthu azidzati, ‘Ngodala azimai ouma, azimai osabala, azimai amene sadayamwitseko mwana.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Pakuti nthawi idzabwera imene inu mudzati, ‘Ndi odala amayi osabereka, mimba zimene sizinabereke ndi mawere amene sanayamwitse!’ Onani mutuwo |