Luka 23:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo unamtsata unyinji waukulu wa anthu, ndi wa akazi amene anadziguguda pachifuwa, namlirira Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo unamtsata unyinji waukulu wa anthu, ndi wa akazi amene anadziguguda pachifuwa, namlirira Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Anthu ambirimbiri ankamutsatira. Pakati pao panalinso akazi amene ankadzigunda pa chifuwa ndi chisoni nkumalira chifukwa cha Iye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Gulu lalikulu la anthu linamutsata Iye, kuphatikiza amayi amene ankabuma ndi kumulirira. Onani mutuwo |