Luka 23:21 - Buku Lopatulika21 koma iwo anafuula, nanena, Mpachikeni, mpachikeni pamtanda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 koma iwo anafuula, nanena, Mpachikeni, mpachikeni pamtanda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma iwo adafuulirafuulira kuti, “Mpachikeni! Mpachikeni!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Koma iwo anapitirirabe kufuwula kuti, “Mpachikeni! Mpachikeni!” Onani mutuwo |